Luke 24:50 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atatero Yesu adaŵatsogolera kuchokera mumzindamo mpaka ku mudzi wa Betaniya. Kumeneko adakweza manja ake naŵadalitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatuluka nao kufikira ku Betaniya; nakweza manja ake, nawadalitsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye atawatengera kunja kwa mzindawo mpaka ku Betaniya, anakweza manja ake ndi kuwadalitsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaturuka nao kufikira ku Betaniya; nakweza manja ace, nawadalitsa.