Luke 24:51 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akuŵadalitsa choncho, adalekana nawo, natengedwa kupita Kumwamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, pakuwadalitsa Iye analekana nao, natengedwa kunka Kumwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye akuwadalitsa, anawasiya ndipo anatengedwa kupita kumwamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, 13 pakuwadalitsa iye analekana nao, natengedwa kunka Kumwamba.