Luke 24:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sali muno ai, wauka. Kumbukirani zimene adaakuuzani akadali ku Galileya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Palibe kuno Iye, komatu anauka; kumbukirani muja adalankhula nanu, pamene analinso m'Galileya,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye sali muno ayi. Wauka! Kumbukirani zimene anakuwuzani pamene anali nanu ku Galileya:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Palibe kuno iye, komatu anauka; kumbukilani muja adalankhula nanu, pamene analinso m'Galileya,