Luke 24:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo atabwerako kumanda kuja, adasimbira zonsezo ophunzira khumi ndi mmodzi aja, ndi anthu ena onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nabwera kuchokera kumanda, nafotokozera zonse khumi ndi mmodziwo, ndi otsala onse omwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atabwerera kuchokera ku mandako, anafotokoza zinthu zonse kwa khumi ndi mmodziwo ndi kwa ena onse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nafotokozera zonse khumi ndi mmodziwo, ndi otsala onse omwe.