Luke 3:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chopetera chake chili m'manja kuti apete tirigu wake. Tsono adzathira tirigu m'nkhokwe, koma mankhusu adzaŵatentha m'moto wosazimika.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amene chouluzira chake chili m'dzanja lake, kuti ayeretse padwale pake, ndi kusonkhanitsa tirigu m'nkhokwe yake; koma mankhusu adzatentha m'moto wosazima.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼdzanja lake muli chopetera kuti ayeretse powomberapo tirigu ndi kusonkhanitsa tirigu ndipo adzatentha zotsalira zonse ndi moto wosazimitsika.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
amene couluzira cace ciri m'dzanja lace, kuti ayeretse padwale pace, ndi kusonkhanitsa tirigu m'ciruli cace; koma mankhusu adzatentha m'moto wosazima.