Luke 3:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yohane ankalalikira anthu Uthenga Wabwino pakuŵalangiza motero, ndiponso mwa njira zina zambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Choteretu iye anauza anthu Uthenga Wabwino ndi kuwadandaulira zinthu zina zambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ndi mawu ena ambiri, Yohane anawachenjeza anthu ndi kuwalalikira Uthenga Wabwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Coteretu iye anauza anthu Uthenga Wabwino ndi kuwadandaulira zinthu zina zambiri.