Luke 3:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komanso adadzudzula mfumu Herode chifukwa chokwatira Herodiasi, mkazi wa mbale wake, ndiponso chifukwa cha zoipa zina zambiri zimene ankachita.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Herode mfumu ija, m'mene Yohane anamdzudzula chifukwa cha Herodiasi, mkazi wa mbale wake, ndi cha zinthu zonse zoipa Herode anazichita,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma pamene Yohane anadzudzula Herode wolamulirayo chifukwa chokwatira Herodia, mkazi wa mʼbale wake, ndi zoyipa zina zonse anazichita,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Herode mfumu ija, m'mene Yohane anamdzudzula cifukwa ca Herodiya, mkazi wa mbale wace, ndi ca zinthu zonse zoina Herode anazicita,