Luke 4:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Malembo akuti, “ ‘Mulungu adzalamula angelo ake kuti akusamaleni.’ Ndiponso,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti kwalembedwa kuti, Adzalamula angelo ake za iwe, kuti akutchinjirize.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti kwalembedwa, “Adzalamulira angelo ake za iwe kuti akutchinjirize mosamala;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti kwalembedwa, kuti, Adzalamulira angelo ace za, iwe, kuti akucinjirize,