Luke 4:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Satana atatha kumuyesa mwa zonsezi, adalekana naye, kudikira nthaŵi ina.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mdierekezi, m'mene adamaliza mayesero onse, analekana naye kufikira nthawi ina.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mdierekezi atamaliza mayesero awa onse, anamusiya Iye kufikira atapeza mpata wina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mdierekezi, m'mene adamariza mayesero onse, analekana naye kufikira nthawi yina.