Luke 4:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
masiku makumi anai, ndipo kumeneko Satana ankamuyesa. Yesu sankadya kanthu masiku amenewo, ndipo pamene masikuwo adatha, adamva njala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kukayesedwa ndi mdierekezi masiku makumi anai. Ndipo Iye sanadye kanthu masiku awo; ndipo pamene anatha anamva njala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kumene anayesedwa ndi mdierekezi masiku makumi anayi. Sanadye kena kalikonse pa masiku amenewo, ndipo pa mapeto pake anamva njala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye sanadya kanthu masiku awo; ndipo pamene anatha anamva njala.