Luke 4:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'nyumba yamapempheroyo munali munthu wogwidwa ndi mzimu womuipitsa. Adalankhula mokuwa kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo munali m'sunagoge munthu, wokhala nacho chiwanda chonyansa; nafuula ndi mau olimba, kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼsunagogemo munali munthu wogwidwa ndi mzimu woyipa. Iye analira ndi mawu akulu, akuti
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo munali m'sunagoge munthu, wokhala naco ciwanda conyansa; napfuula ndi mau olimba, kuti,