Luke 4:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho mukandipembedza, zonsezi zidzakhala zanu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake ngati Inu mudzagwadira pamaso panga, wonsewo udzakhala wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati mutandilambira, zonsezi zidzakhala zanu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace ngati Inu mudzagwadira pamaso panga, wonsewo udzakhala wanu.