Luke 5:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Iye adapita kumalo kosapitapita anthu, namakapemphera kumeneko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Iye anazemba, nanka m'mapululu, nakapemphera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yesu nthawi zambiri ankachoka kupita ku malo a yekha kukapemphera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iye anazemba, nanka m'mapululu, nalikupemphera.