Luke 5:39 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ndipo munthu akangolaŵa vinyo wakale, watsopano sangamufune. Pajatu amati, ‘Wakale ndiye vinyo chaiye.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo palibe munthu atamwa vinyo wakale afuna watsopano; pakuti anena, Wakale ali wokoma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo palibe amene atamwa vinyo wakale amafuna watsopano, pakuti amati, ‘Wakale ndi okoma.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo palibe munthu atamwa vinyo wakale afuna watsopano; pakuti anena, Wakale ali wokoma.