Luke 5:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono iwo adaponyadi makoka, napha nsomba zambirimbiri, kotero kuti makokawo ankayamba kung'ambika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene anachita ichi, anazinga unyinji waukulu wa nsomba; ndipo makoka ao analinkung'ambika;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atachita izi, anagwira nsomba zambiri kotero kuti makhoka awo anayamba kungʼambika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene anacita ici, anazinga unyinji waukuru wansomba; ndipo makoka ao analinkung'ambika;