Luke 6:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa tsiku lina la Sabata Yesu ankadutsa m'minda ya tirigu. Ophunzira ake ankathyolako ngala za tirigu, namazifikisa ndi manja, nkumadya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali tsiku la Sabata, Iye analinkupita pakati pa minda ya tirigu; ndipo ophunzira ake analinkubudula ngala za tirigu, nazifikisa m'manja mwao, nadya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku lina la Sabata Yesu ankadutsa mʼminda yatirigu, ndipo ophunzira ake anayamba kubudula ngala zatirigu, namazifikisa mʼmanja mwawo ndi kumadya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali tsiku la Sabata, iye analinkupita pakati pa minda ya tirigu; ndipo ophunzira ace analinkubudula ngala za tirigu, nazifikisa m'manja mwao, nadya.