Luke 6:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Afarisi ena adafunsa kuti, “Bwanji mukuchita zimene siziloledwa pa tsiku la Sabata?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Afarisi ena anati, Muchitiranji chosaloledwa kuchitika tsiku la Sabata?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ena mwa Afarisi anafunsa kuti, “Kodi nʼchifukwa chiyani mukuchita zosaloledwa pa tsiku la Sabata?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Afarisi ena anati, Mucitiranji cosaloledwa kucitika tsiku la Sabata?