Luke 6:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Koma ndinu atsoka, anthu achumanu, chifukwa mwalandiriratu zokusangalatsani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma tsoka inu eni chuma! Chifukwa mwalandira chisangalatso chanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndinu atsoka, anthu olemera, popeza mwalandiriratu zokusangalatsani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma tsoka inu eni cuma! cifukwa mwalandira cisangalatso canu.