Luke 6:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Koma inu amene mukumva mau anga, ndikukuuzani kuti, Muzikonda adani anu, muziŵachitira zabwino amene amadana nanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ndinena kwa inu akumva, Kondanani nao adani anu; chitirani zabwino iwo akuda inu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma Ine ndikuwuza inu amene mukundimva: Kondani adani anu, chitirani zabwino amene amakudani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ndinena kwa inu akumva, Kondanani nao adani anu; citirani zabwino iwo akuda inu,