Luke 6:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu akakupempha kanthu, uzimpatsa. Ndipo munthu akatenga zinthu zako, usamlamule kuti abweze.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu aliyense akakupempha kanthu, umpatse; ndi iye amene alanda zako, usazipemphanso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mupatseni aliyense amene akupemphani kanthu ndipo ngati wina atenga chinthu chanu, musamulamule kuti akubwezereni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu ali yense akakupempha kanthu, umpatse; ndi iye amene alanda zako, usazipemphanso.