Luke 6:46 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Bwanji mumangoti, ‘Ambuye, Ambuye,’ koma chonsecho simuchita zimene ndimanena?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo munditchuliranji Ine, Ambuye, Ambuye, ndi kusachita zimene ndizinena?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kodi nʼchifukwa chiyani munditchula kuti, ‘Ambuye, Ambuye’ koma simuchita zimene Ine ndinena?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo 14 mundichuliranji Ine, Ambuye, Ambuye, ndi kusacita zimene ndizinena?