Luke 6:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yesu popitiriza adaŵauza kuti, “Mwana wa Munthu ali ndi ulamuliro wonse pa zokhudza tsiku la Sabata.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Iye ananena kwa iwo, kuti, Mwana wa Munthu ali Mbuye wa tsiku la Sabata.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Yesu anawawuza kuti, “Mwana wa Munthu ndi Ambuye wa Sabata.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye ananena kwa iwo, kuti, Mwana wa munthu ali Mbuye wa tsiku la Sabata.