Luke 7:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Yesu adapita ku mudzi wina, dzina lake Naini. Ophunzira ake pamodzi ndi anthu ena ambirimbiri adatsagana naye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, katapita kamphindi, Iye anapita kumudzi, dzina lake Naini; ndipo ophunzira ake ndi mpingo waukulu wa anthu anapita naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zitangotha izi, Yesu anapita ku mudzi wa Naini ndipo ophunzira ake ndi gulu lalikulu la anthu linapita naye pamodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, katapita kamphindi, iye ana pita kumudzi, dzina lace Nayini; ndipo ophunzira ace ndi mpingo waukuru wa anthu anapita nave.