Luke 7:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Ambuye adamuwona, adamumvera chisoni, namuuza kuti, “Mai, musalire.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene Ambuye anamuona, anagwidwa ndi chifundo chifukwa cha iye, nanena naye, Usalire.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ambuye atamuona mayiyo, mtima wawo unagwidwa naye chifundo ndipo anati, “Usalire.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene Ambuye anamuona, anagwidwa ndi cifundo cifukwa ca iye, nanena naye, Usalire.