Luke 7:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo wakufayo adakhala tsonga nayamba kulankhula, Yesu nkumupereka kwa mai wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo wakufayo anakhala tsonga, nayamba kulankhula. Ndipo anampereka kwa amake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wakufayo anakhala tsonga ndi kuyamba kuyankhula, ndipo Yesu anamupereka mnyamatayo kwa amayi ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo wakufayo anakhala tsonga, nayamba kulankhula. Ndipo anampereka kwa amace.