Luke 7:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono iye adaitanapo ophunzira ake ena aŵiri, naŵatuma kwa Ambuye kukaŵafunsa kuti, “Kodi Inu ndinu uja ankati adzabwerayu, kapena tiziyembekezera wina?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yohane anaitana awiri a ophunzira ake, nawatuma kwa Ambuye, nanena, Kodi ndinu wakudzayo, kapena tiyang'anire wina?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
anawatumiza kwa Ambuye kukafunsa kuti, “Kodi ndinu anayenera kubwerayo, kapena tiyembekezere wina?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yohane anaitana awiri a ophunzira ace, nawatuma kwa Ambuye, nanena, Kodi ndinu wakudzayo, kapena tiyang'anire wina?