Luke 7:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tanenanitu, mudaati mukaona chiyani? Mneneri kodi? Zoonadi, ndipo ndikunenetsa kuti mudakaona woposa mneneri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma munatuluka kukaona chiyani? Mneneri kodi? Etu, ndinena kwa inu, ndipo wakuposa mneneri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma inu munkapita kukaona chiyani? Mneneri? Inde, Ine ndikukuwuzani, woposa mneneri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma munaturuka kukaona ciani? Mneneri kodi? Etu, ndinena kwa inu, ndipo wakuposa mneneri.