Luke 7:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu onse, ndi okhometsa msonkho omwe, adamva mau a Yohane, ndipo pakubatizidwa ndi Yohaneyo adavomereza kuti Mulungu ngwolungama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu onse ndi amisonkho omwe, pakumva, anavomereza kuti Mulungu ali wolungama, popeza anabatizidwa iwo ndi ubatizo wa Yohane.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu onse, ngakhale amisonkho, atamva mawu a Yesu, anavomereza kuti njira ya Mulungu ndi yolondola, chifukwa anabatizidwa ndi Yohane.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu onse ndi amisonkho omwe, pakumva, anabvomereza kuti Mulungu ali wolungama, popeza anabatizidwa iwo ndi ubatizo wa Yohane.