Luke 7:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Kaya anthu amakonoŵa ndingaŵafanizire ndi chiyani? Ali ngati chiyani?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo, ndidzafanizira ndi chiyani anthu a mbadwo uno? Ndipo afanana ndi chiyani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kodi ndingawafanizire chiyani anthu a mʼbado uno? Ali ngati chiyani?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo, ndidzafanizira ndi ciani anthu a mbadwo uno? ndipo afanana ndi ciani?