Luke 7:43 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Simoni adati, “Ndiyesa koma amene adamkhululukira zambiri uja.” Yesu adamuuza kuti, “Wayankha bwino.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Simoni anayankha, nati, Ndiyesa kuti, iye amene anamkhululukira zoposa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Simoni anayankha kuti, “Ndikuganiza kuti ndi amene anamukhululukira ngongole yayikulu.” Yesu anati, “Wayankha molondola.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Simoni anayankha, nati, Ndiyesa kuti, iye amene anamkhululukira zoposa,