Luke 7:49 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo amene ankadya naye adayamba kudzifunsa mumtima mwao kuti, “Kodi ndani uyu wokhululukira ndi machimo omweyu?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwo akuseama naye pachakudya anayamba kunena mwa okha, Uyu ndani amene akhululukiranso machimo?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Alendo enawo anayamba kumanena mʼmitima mwawo kuti, “Uyu ndi ndani amene akhululukiranso machimo?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwo akuseama naye pacakudya anayamba kunena mwa okha, Uyu ndani amene akhululukiranso macimo?