Luke 8:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Oŵeta nkhumbazo ataona zimenezi, adathaŵa, nakauza anthu ku mzinda ndi ku midzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo akuwetawo m'mene anaona chimene chinachitika, anathawa, nauza akumudzi ndi kumilaga yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Oweta nkhumbazo ataona zimene zinachitikazo, anathamanga ndi kukanena izi mu mzinda ndi ku madera a ku midzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo akuwetawo m'mene anaona cimene cinacitika, anathawa, nauza a kumudzi ndi kumiraga yace.