Luke 8:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ambirimbiri ochokera ku midzi yonse adasonkhana kumene kunali Yesu. Tsono Iye adaŵaphera fanizo. Adati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene khamu lalikulu la anthu linasonkhana, ndi anthu a kumidzi yonse anafika kwa Iye, anati mwa fanizo:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu ambiri ankasonkhana, ndipo pamene anthu ankabwera kwa Yesu kuchokera ku midzi, Iye anawawuza fanizo ili,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene khamu lalikuru la anthu linasonkhana, ndi anthu a ku midzi yonse anafika kwa iye, anati mwa fanizo: