Luke 8:53 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo anthuwo adayamba kumseka monyodola, chifukwa ankadziŵa kuti mwanayo wamwalira basi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamseka Iye pwepwete podziwa kuti anafa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anamuseka podziwa kuti anali atamwalira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamseka iye pwepwete podziwa kuti anafa.