Luke 8:54 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesu adagwira mwanayo pa dzanja nanena mokweza mau kuti, “Mwana iwe, dzuka!”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Iye anamgwira dzanja lake, naitana, nati, Buthu, tauka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Iye anamugwira dzanja lake ndipo anati, “Mwana wanga, dzuka!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye anamgwira dzanja lace, naitana, nati, Buthu, tauka.