Luke 8:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mbeu zina zidagwera pa zitsamba zaminga. Zitsambazo pokula zidalanda chakudya cha mbeu zija.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo zina zinagwa pakati pa minga; ndi mingayo inaphuka pamodzi nazo, nizitsamwitsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mbewu zina zinagwera pakati pa minga, zinakulira pamodzi ndi mingazo ndipo zinalepheretsa mmerawo kukula.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo zina zinagwa pakati pa minga; ndi mingayo inapuka pamodzi nazo, nizitsamwitsa.