Luke 9:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Yesu adaŵafunsa kuti, “Nanga inuyo, mumati ndine yani?” Petro adayankha kuti, “Inu ndinu Mpulumutsi wolonjezedwa uja wa Mulungu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati kwa iwo, Koma inu munena kuti Ine ndine yani? Ndipo anayankha Petro, nati, Khristu wa Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anafunsa kuti, “Koma nanga inu mumati Ine ndine yani?” Petro anayankha kuti, “Mpulumutsi wolonjezedwa uja wa Mulungu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati kwa iwo, Koma inu munena kuti Ine ndine yani? Ndipo anayankha Petro, nati, Kristu wa Mulungu.