Luke 9:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesu adalamula ophunzira ake kuti asauze munthu wina aliyense zimenezi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Iye anawauzitsa iwo, nalamulira kuti asanene ichi kwa munthu aliyense;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yesu anawachenjeza kwambiri kuti asawuze wina aliyense za izi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye anawauzitsa iwo, nalamulira kuti asanene ici kwa munthu ali yense;