Luke 9:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Patapita ngati masiku asanu ndi atatu atanena mau ameneŵa, Yesu adatenga Petro, Yohane ndi Yakobe, nakwera nawo ku phiri kukapemphera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene padatha ngati masiku asanu ndi atatu atanena mau amenewa, Iye anatenga Petro ndi Yohane ndi Yakobo apite naye, nakwera m'phiri kukapemphera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Patatha pafupifupi masiku asanu ndi atatu Yesu atanena izi, Iye anatenga Petro, Yohane ndi Yakobo ndi kukwera ku phiri kukapemphera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene padatha ngati masiku asanu ndi atatu atanena mau amenewa, Iye anatenga Petro ndi Yohane ndi Yakobo apite naye, nakwera m'phiri kukapemphera.