Luke 9:37 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'maŵa mwake Yesu ndi ophunzira atatuwo adatsika kuphiri kuja, ndipo anthu ambirimbiri adadzamchingamira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali, m'mawa mwake, atatsika m'phiri, khamu lalikulu la anthu linakomana naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mmawa mwake, akutsika ku phiri, anthu ambiri anakumana naye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali, m'mawa mwace, atatsika m'phiri, khamu lalikuru la anthu linakomana naye.