Luke 9:44 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mumvetse bwino zimene ndikuuzenizi: Mwana wa Munthu akudzaperekedwa kwa anthu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Alowe mau amenewa m'makutu anu; pakuti Mwana wa Munthu adzaperekedwa m'manja a anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tamvetsetsani zimene ndikufuna kukuwuzani: Mwana wa Munthu akupita kukaperekedwa mʼmanja mwa anthu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Alowe mau ame: newa m'makutu anu; pakuti Mwana wa munthu adzaperekedwa m'manja a anthu.