Luke 9:45 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwowo sadamvetse mau ameneŵa. Anali obisika kwa iwo, kotero kuti sadaŵamvetsetse. Koma ankaopa kumufunsa zimenezi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iwo sanadziwitse mau awa, ndipo anabisidwa kwa iwo, kuti asawadziwe; ndipo anaopa kumfunsa za mau awa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma iwo sanazindikire zimene amatanthauza. Izi zinawadabwitsa kotero sanathe kuzimvetsa ndipo anaopa kumufunsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iwo sanadziwitse mau awa, ndipo anabisidwa kwa iwo, kuti asawadziwe; ndipo anaopa kumfunsa za mau awa.