Luke 9:46 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ophunzira adayamba kutsutsana zakuti wamkulu ndani pakati pao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anayamba kutsutsana kuti wamkulu mwa iwo ndani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mkangano unayambika pakati pa ophunzira wa kuti wamkulu koposa akanakhala ndani mwa iwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anayamba kutsutsana kuti wamkulu mwa iwo ndani.