Luke 9:50 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Yesu adamuuza kuti, “Musamletse ai, chifukwa wosatsutsana nanu, ngwogwirizana nanu ameneyo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Yesu anati kwa iye, Musamletse, pakuti iye amene satsutsana nanu athandizana nanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yesu anati, “Wosamuletsa, pakuti amene satsutsana nanu ali mbali yanu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Yesu anati kwa iye, Musamletse, pakuti iye amene satsutsana nanu athandizana nanu.