Luke 9:51 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene masiku ankayandikira oti Yesu atengedwe kunka Kumwamba, Iye adatsimikiza ndithu zopita ku Yerusalemu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali, pamene anayamba kukwanira masiku akuti alandiridwe Iye kumwamba, Yesu anatsimikiza kuloza nkhope yake kunka ku Yerusalemu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthawi itayandikira yoti Iye atengedwe kupita kumwamba, Yesu anatsimikiza zopita ku Yerusalemu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali, pamene anayamba kukwanira masiku akuti alandiridwe iye kumwamba, Yesu anatsimika kuloza nkhope yace kunka ku Yerusalemu,