Luke 9:52 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero adatuma amithenga kuti atsogole, akaloŵe m'mudzi wina wa Asamariya kukamkonzera malo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
natumiza amithenga patsogolo pake; ndipo ananka, nalowa m'mudzi wa Asamariya, kukamkonzera Iye malo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo anatuma nthumwi kuti zitsogole. Iwo anapita mʼmudzi wa Asamariya kuti akonzekere kumulandira,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
natumiza amithenga patsogolo pace; ndipo ananka, nalowa m'mudzi wa Asamariya, kukamkonzera iye malo.