Luke 9:53 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu am'mudzimo sadafune kumlandira, chifukwa Iye ankapita ku Yerusalemu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwo sanamlandire Iye, chifukwa nkhope yake inali yoloza kunka ku Yerusalemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
koma anthu kumeneko sanamulandire chifukwa Iye ankapita ku Yerusalemu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwo sanamlandira iye, cifukwa nkhope yace inali yoloza kunka ku Yerusalemu.