Luke 9:60 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesu adamuuza kuti, “Aleke akufa aziika akufa anzao. Koma iwe, kalalike Ufumu wa Mulungu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anati kwa iye, Leka akufa aike akufa a eni okha; koma muka iwe nubukitse mbiri yake ya Ufumu wa Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yesu anati kwa iye, “Aleke akufa ayikane akufa okhaokha, koma iwe pita ukalalikire ufumu wa Mulungu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anati kwa iye, Leka akufa aike akufa a eni okha; koma muka iwe nubukitse mbiri yace ya Ufumu wa Mulungu.