Luke 9:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mfumu Herode atamva zonse zimene zinkachitika zija, zidamuthetsa nzeru, chifukwa ena ankanena kuti, “Ameneyu ndi Yohane Mbatizi uja, adauka kwa akufa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Herode chiwangacho anamva mbiri yake ya zonse zinachitika; ndipo inamthetsa nzeru, chifukwa ananena anthu ena, kuti Yohane anauka kwa akufa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano Herode olamulirayo anamva zonse zimachitikazi. Ndipo iye anavutika kwambiri chifukwa ena amati Yohane waukitsidwa kwa akufa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Herode ciwangaco anamva mbiri yace ya zonse zinacitika; ndipo inamthetsa nzeru, cifukwa ananena anthu ena, kuti Yohane anauka kwa akufa;