Luke 9:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ena ankanena kuti, “Iyai, ameneyu ndi Eliya, waonekanso.” Enanso ankati, “Iyai, koma ndi mmodzi mwa aneneri akale aja, wauka kwa akufa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma ena, kuti Eliya anaoneka; ndipo ena, kuti mneneri wina wa akale aja anauka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ena amati Eliya waonekera, ndipo ena anatinso mmodzi wa aneneri akalekale waukanso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma ena, kuti Eliya anaoneka; ndipo ena, kuti mneneri wina wa akale aja anauka.